Numeri 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iwo anasonkhana n’kuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni, kuti: “Tatopa nanu tsopano! Khamu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga n’chifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”+ Numeri 16:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Nthakayo inatsegula pakamwa pake n’kuwameza iwowo ndi mabanja awo, limodzi ndi anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora, komanso katundu wawo yense.+
3 Choncho iwo anasonkhana n’kuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni, kuti: “Tatopa nanu tsopano! Khamu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga n’chifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”+
32 Nthakayo inatsegula pakamwa pake n’kuwameza iwowo ndi mabanja awo, limodzi ndi anthu ena onse amene anali kumbali ya Kora, komanso katundu wawo yense.+