Numeri 12:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Iwo ankanena kuti: “Kodi Yehova walankhula kudzera kwa Mose yekha? Kodi sanalankhulenso kudzera kwa ife?”+ Koma Yehova anali kumvetsera.+
2 Iwo ankanena kuti: “Kodi Yehova walankhula kudzera kwa Mose yekha? Kodi sanalankhulenso kudzera kwa ife?”+ Koma Yehova anali kumvetsera.+