Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tsopano Miriamu ndi Aroni anayamba kum’nena Mose chifukwa cha mkazi wachikusi amene anam’kwatira.+

  • Numeri 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Ana onse a Isiraeli anayamba kudandaula za Mose ndi Aroni.+ Ndipo khamu lonselo linati: “Zikanakhala bwino tikanangofera ku Iguputo, kapena tikanangofera m’chipululu muno.

  • 1 Samueli 15:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Pakuti kupanduka+ n’chimodzimodzi ndi tchimo la kuwombeza,+ ndipo kuchita zinthu modzikuza n’chimodzimodzi ndi kugwiritsa ntchito mphamvu zamatsenga ndiponso aterafi.+ Popeza iwe wakana mawu a Yehova,+ iyenso wakukana kuti usakhalenso mfumu.”+

  • Salimo 106:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 Iwo anayamba kuchitira Mose kaduka mumsasa,+

      Ndiponso Aroni, woyera wa Yehova.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena