Numeri 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Choncho iwo anasonkhana n’kuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni, kuti: “Tatopa nanu tsopano! Khamu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga n’chifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”+
3 Choncho iwo anasonkhana n’kuyamba kutsutsana+ ndi Mose ndi Aroni, kuti: “Tatopa nanu tsopano! Khamu lonseli ndi loyera,+ ndipo Yehova ali pakati pawo.+ Nanga n’chifukwa chiyani inu mukudzikweza pa mpingo wa Yehova?”+