Numeri 14:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+ Deuteronomo 9:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+ 1 Samueli 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma ngati simudzamvera mawu a Yehova,+ moti n’kupandukiradi malamulo a Yehova,+ dzanja la Yehova lidzatsutsana ndi inu ndi abambo anu.+
9 Chongofunika n’chakuti musam’pandukire Yehova.+ Komanso anthu a m’dzikolo musawaope,+ chifukwa ali ngati chakudya kwa ife. Alibenso chitetezo,+ koma ifeyo Yehova ali nafe.+ Musawaope ayi.”+
7 “Kumbukirani izi: Simuyenera kuiwala mmene munaputira Yehova Mulungu wanu m’chipululu.+ Anthu inu mwasonyeza khalidwe lopandukira Yehova kuyambira tsiku limene munatuluka m’dziko la Iguputo mpaka kudzafika malo ano.+
15 Koma ngati simudzamvera mawu a Yehova,+ moti n’kupandukiradi malamulo a Yehova,+ dzanja la Yehova lidzatsutsana ndi inu ndi abambo anu.+