Salimo 106:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mumsasa, iwo anayamba kuchitira nsanje MoseNdiponso Aroni,+ woyera wa Yehova.+