Salimo 106:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Iwo anayamba kuchitira Mose kaduka mumsasa,+Ndiponso Aroni, woyera wa Yehova.+