Levitiko 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Choncho muzim’patula+ chifukwa ndiye wopereka mkate wa Mulungu wanu. Azikhala woyera kwa inu,+ chifukwa ine Yehova, amene ndikukupatulani, ndine woyera.+ Numeri 16:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 M’zofukizirazo mudzaikemo moto ndiponso zofukiza ndi kubwera nazo pamaso pa Yehova mawa. Munthu amene Yehova ati adzamusankhe,+ ameneyo ndiye woyera. Inenso ndatopa nanu, inu ana a Levi!”+
8 Choncho muzim’patula+ chifukwa ndiye wopereka mkate wa Mulungu wanu. Azikhala woyera kwa inu,+ chifukwa ine Yehova, amene ndikukupatulani, ndine woyera.+
7 M’zofukizirazo mudzaikemo moto ndiponso zofukiza ndi kubwera nazo pamaso pa Yehova mawa. Munthu amene Yehova ati adzamusankhe,+ ameneyo ndiye woyera. Inenso ndatopa nanu, inu ana a Levi!”+