Ekisodo 28:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 “Upangenso kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti, ‘Chiyero n’cha Yehova.’+ Levitiko 11:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Levitiko 20:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 “‘Choncho mudzipatule monga anthu oyera,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu. Yesaya 43:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ine ndine Yehova, Woyera wanu,+ Mlengi wa Isiraeli+ ndiponso Mfumu yanu.”+
36 “Upangenso kachitsulo konyezimira kaphanthiphanthi kagolide woyenga bwino, ndipo ulembepo mochita kugoba ngati mmene amagobera chidindo, mawu akuti, ‘Chiyero n’cha Yehova.’+
45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+