Levitiko 11:45 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:45 Nsanja ya Olonda,5/15/2004, tsa. 23
45 Ine ndine Yehova amene ndinakutulutsani mʼdziko la Iguputo kuti ndikusonyezeni kuti ndine Mulungu.+ Muzikhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+