Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 22:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 “Inuyo muzikhala anthu oyera pamaso panga+ ndipo musadye nyama imene yaphedwa ndi chilombo kuthengo.+ Imeneyo muziponyera agalu.+

  • Levitiko 20:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Choncho mudzipatule monga anthu oyera,+ chifukwa ine ndine Yehova Mulungu wanu.

  • Levitiko 20:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Mukhale oyera kwa ine,+ chifukwa ine Yehova ndine woyera.+ Ine ndikukupatulani kwa anthu a mitundu ina kuti mukhale anthu anga.+

  • Numeri 15:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndakupatsani lamulo limeneli kuti muzikumbukira ndi kusunga malamulo anga onse, ndi kukhaladi oyera kwa Mulungu wanu.+

  • Deuteronomo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena