Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+ Numeri 15:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Ndakupatsani lamulo limeneli kuti muzikumbukira ndi kusunga malamulo anga onse, ndi kukhaladi oyera kwa Mulungu wanu.+ 1 Petulo 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma khalani motsanzira Woyera amene anakuitanani. Inunso khalani oyera m’makhalidwe anu onse,+
2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+
40 Ndakupatsani lamulo limeneli kuti muzikumbukira ndi kusunga malamulo anga onse, ndi kukhaladi oyera kwa Mulungu wanu.+