Levitiko 11:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi. Aefeso 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+ 1 Petulo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 chifukwa Malemba amati: “Mukhale oyera, chifukwa ine ndine woyera.”+
44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.
4 Wachita zimenezi monga mmene anatisankhira+ kuti tikakhale ogwirizana ndi Yesuyo dziko lisanakhazikitsidwe,+ kuti tikakhale oyera ndi opanda chilema+ pamaso pa Mulungu m’chikondi.+