Levitiko 11:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi. Levitiko 19:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+ Levitiko 20:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Mukhale oyera kwa ine,+ chifukwa ine Yehova ndine woyera.+ Ine ndikukupatulani kwa anthu a mitundu ina kuti mukhale anthu anga.+ Deuteronomo 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+
44 Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Mudzipatule ndi kukhala oyera,+ chifukwa ine ndine woyera.+ Choncho musamadzidetse ndi chamoyo chilichonse choyenda padziko lapansi.
2 “Uza khamu lonse la ana a Isiraeli kuti, ‘Mukhale oyera,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wanu ndine woyera.+
26 Mukhale oyera kwa ine,+ chifukwa ine Yehova ndine woyera.+ Ine ndikukupatulani kwa anthu a mitundu ina kuti mukhale anthu anga.+
14 Pakuti Yehova Mulungu wanu akuyendayenda mumsasa wanu kuti akulanditseni+ ndi kupereka adani anu m’manja mwanu.+ Choncho msasa wanu uzikhala woyera,+ kuti asaone choipa chilichonse pakati panu ndi kutembenuka n’kuleka kuyenda nanu limodzi.+