Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 46:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ineyo ndipita nawe ku Iguputo, ndiponso ine ndi amene ndidzabwere nawe kuchokera kumeneko.+ Ndipo Yosefe ndi amene adzakutseke maso pa imfa yako.”+

  • Ekisodo 6:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Chotero ndidzakutengani kukhala anthu anga,+ ndi kukusonyezani kuti ndine Mulungu.+ Inuyo mudzadziwadi kuti ine ndine Yehova Mulungu wanu, amene ndidzakutulutsani mu Iguputo, ndi kukuchotserani goli lawo.+

  • Ekisodo 29:46
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 46 Iwo adzadziwa kuti ine ndine Yehova Mulungu wawo, amene ndinawatulutsa m’dziko la Iguputo kuti ndikhale pakati pawo.+ Ine ndine Yehova Mulungu wawo.+

  • Salimo 81:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ine Yehova, ndine Mulungu wanu,+

      Amene ndinakutulutsani m’dziko la Iguputo.+

      Tsegulani pakamwa panu ndipo ndidzaikamo chakudya.+

  • Hoseya 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Pa nthawi imene Isiraeli anali mnyamata ndinamukonda,+ ndipo ndinaitana mwana wangayu kuti atuluke mu Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena