Ekisodo 4:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Choncho ukamuuze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+ Mateyu 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 ndipo anakhala kumeneko mpaka kumwalira kwa Herode, kuti zimene Yehova analankhula kudzera mwa mneneri wake zikwaniritsidwe.+ Iye anati: “Ndinaitana mwana wangayu kuti atuluke mu Iguputo.”+
22 Choncho ukamuuze Farao kuti, ‘Yehova wanena kuti: “Isiraeli ndi mwana wanga wamwamuna, mwana wanga woyamba kubadwa.+
15 ndipo anakhala kumeneko mpaka kumwalira kwa Herode, kuti zimene Yehova analankhula kudzera mwa mneneri wake zikwaniritsidwe.+ Iye anati: “Ndinaitana mwana wangayu kuti atuluke mu Iguputo.”+