Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+

  • Deuteronomo 14:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Pakuti ndinu anthu oyera+ kwa Yehova Mulungu wanu, ndipo Yehova wakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera,+ mwa anthu onse okhala padziko lapansi.

  • Yeremiya 31:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Adzabwera akulira,+ ndipo ndidzayankha kuchonderera kwawo kuti ndiwakomere mtima. Ndidzawayendetsa kupita kuzigwa za madzi.+ Ndidzawayendetsa m’njira zabwino mmene sadzapunthwa. Pakuti ine ndakhala Tate wa Isiraeli,+ ndipo Efuraimu ndi mwana wanga wamwamuna woyamba kubadwa.”+

  • Hoseya 11:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Pa nthawi imene Isiraeli anali mnyamata ndinamukonda,+ ndipo ndinaitana mwana wangayu kuti atuluke mu Iguputo.+

  • Aroma 9:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Amenewa ndi Aisiraeli,+ amene Mulungu anawatenga kukhala ana ake.+ Anawapatsanso ulemerero,+ mapangano,+ Chilamulo,+ utumiki wopatulika+ ndi malonjezo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena