Machitidwe 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 “Chotero ife tikulengeza kwa inu uthenga wabwino wa lonjezo limene linaperekedwa kwa makolo athu.+ Aroma 4:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pakuti Abulahamu kapena mbewu yake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti anali wolungama mwa chikhulupiriro.+
32 “Chotero ife tikulengeza kwa inu uthenga wabwino wa lonjezo limene linaperekedwa kwa makolo athu.+
13 Pakuti Abulahamu kapena mbewu yake sanalonjezedwe kuti adzalandira dziko monga cholowa chawo chifukwa cha chilamulo ayi.+ Analandira lonjezolo chifukwa chakuti anali wolungama mwa chikhulupiriro.+