Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 7:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+ Deuteronomo 26:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipo lero Yehova wakuchititsani kunena kuti mudzakhala anthu ake, chuma chapadera,+ monga mmene anakulonjezerani,+ ndiponso kuti mudzasunga malamulo ake onse,
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
6 Pakuti ndinu anthu oyera kwa Yehova Mulungu wanu.+ Yehova Mulungu wanu anakusankhani kuti mukhale anthu ake, chuma chake chapadera, mwa anthu onse okhala padziko lapansi.+
18 Ndipo lero Yehova wakuchititsani kunena kuti mudzakhala anthu ake, chuma chapadera,+ monga mmene anakulonjezerani,+ ndiponso kuti mudzasunga malamulo ake onse,