Machitidwe 26:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ndipo mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli, mwa kumuchitira utumiki wopatulika mosalekeza usana ndi usiku.+ Chotero Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+ Aheberi 9:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Tsopano, pangano loyamba lija linali ndi malamulo ake a utumiki wopatulika+ ndiponso malo ake oyera a padziko lapansi.+
7 Ndipo mafuko athu 12 akuyembekezera kuona kukwaniritsidwa kwa lonjezo limeneli, mwa kumuchitira utumiki wopatulika mosalekeza usana ndi usiku.+ Chotero Mfumu, Ayuda akundiimba mlandu chifukwa cha chiyembekezo chimenechi.+
9 Tsopano, pangano loyamba lija linali ndi malamulo ake a utumiki wopatulika+ ndiponso malo ake oyera a padziko lapansi.+