Yoswa 24:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ndiyeno Yoswa anauza anthuwo kuti: “Simungathe kutumikira Yehova, chifukwa iye ndi Mulungu woyera.+ Iye ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha.+ Iye sadzakhululuka machimo anu ndi kupanduka kwanu.+ 1 Samueli 2:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+ 1 Samueli 6:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako amuna a ku Beti-semesi ananena kuti: “Ndani angaime pamaso pa Yehova Mulungu woyera,+ ndipo kodi sangatileke n’kupita kwa ena?”+
19 Ndiyeno Yoswa anauza anthuwo kuti: “Simungathe kutumikira Yehova, chifukwa iye ndi Mulungu woyera.+ Iye ndi Mulungu amene amafuna kuti anthu azidzipereka kwa iye yekha.+ Iye sadzakhululuka machimo anu ndi kupanduka kwanu.+
2 Palibe woyera ngati Yehova. Palibe aliyense koma inu nokha.+Palibe thanthwe lofanana ndi Mulungu wathu.+
20 Kenako amuna a ku Beti-semesi ananena kuti: “Ndani angaime pamaso pa Yehova Mulungu woyera,+ ndipo kodi sangatileke n’kupita kwa ena?”+