Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 23:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Samala ndipo umvere mawu ake. Usam’pandukire, chifukwa sadzalekerera zolakwa zanu,+ pakuti dzina langa lili mwa iye.

  • Numeri 14:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 “‘“Ine Yehova ndalankhula, mudzandifunse ngati sindidzawafafaniza m’chipululu mommuno anthu oipa onsewa,+ amene agwirizana kuti atsutsane ndi ine. Onse adzathera m’chipululu mommuno.+

  • 1 Samueli 3:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 N’chifukwa chake ndalumbirira a m’nyumba ya Eli kuti mpaka kalekale sadzapewa chilango chifukwa cha cholakwa cha anthu a m’nyumba yakewo, ngakhale atapereka nsembe.”+

  • 2 Petulo 2:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Chotero, zimenezi zikusonyeza kuti Yehova amadziwa kupulumutsa anthu odzipereka kwa iye akakhala pa mayesero.+ Koma anthu osalungama amawasungira tsiku loweruza kuti adzawawononge,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena