Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 5:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Usaziweramire kapena kuzitumikira,+ chifukwa ine Yehova Mulungu wako, ndine Mulungu wofuna kuti anthu azidzipereka kwa ine ndekha,*+ wolanga ana, zidzukulu ndi ana a zidzukuluzo,* chifukwa cha zolakwa za anthu odana ndi ine.+

  • 1 Samueli 2:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Musatero+ ana anga, chifukwa nkhani imene ndikumva, imene anthu a Yehova akufalitsa, si yabwino ayi.+

  • 1 Samueli 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Ngakhalenso likasa la Mulungu linalandidwa,+ ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anafa.+

  • 1 Samueli 22:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Ndiyeno Abiyatara anauza Davide kuti: “Sauli wapha ansembe a Yehova.”

  • 1 Mafumu 2:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Choncho Solomo anathamangitsa Abiyatara n’kumusiyitsa kutumikira monga wansembe wa Yehova, pokwaniritsa mawu amene Yehova analankhula ku Silo,+ otsutsana ndi nyumba ya Eli.+

  • Aheberi 10:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Pakuti ngati tikuchita machimo mwadala+ pambuyo podziwa choonadi molondola,+ palibe nsembe ina yotsala imene ingaperekedwe chifukwa cha machimo athuwo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena