Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 2:31
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 31 Tsopano imva izi, masiku adzafika pamene ndidzadula dzanja lako ndi la nyumba ya kholo lako, moti m’nyumba yako simudzakhala munthu wokalamba.+

  • 1 Samueli 2:34
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 34 Ndipo chizindikiro chako chimene chidzachitikira ana ako awiri Hofeni ndi Pinihasi+ ndi ichi: Onse awiri adzafa tsiku limodzi.+

  • 1 Samueli 4:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Choncho munthu wobweretsa uthengayo anayankha kuti: “Aisiraeli athawa pamaso pa Afilisiti, ndipo agonjetsedwa koopsa.+ Ana anunso awiri, Hofeni ndi Pinihasi,+ aphedwa. Ngakhalenso likasa la Mulungu woona lalandidwa.”+

  • Salimo 78:64
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 64 Ansembe ake anagwa ndi lupanga,+

      Ndipo akazi awo amasiye sanalire.+

  • Mlaliki 8:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Palibe munthu amene ali ndi mphamvu pa mzimu kuti auletse mzimuwo.+ Palibenso amene ali ndi mphamvu pa tsiku la imfa.+ Palibe amene samenya nawo nkhondo,+ ndipo kuchita zoipa sikudzapulumutsa amene amachita zoipawo.+

  • Mlaliki 8:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma woipayo sizidzamuyendera bwino n’komwe,+ ndiponso sadzachulukitsa masiku ake amene ali ngati mthunzi,+ chifukwa saopa Mulungu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena