1 Samueli 2:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma pali munthu wa m’nyumba yako amene sindidzamuchotsa paguwa langa lansembe kuti achititse maso ako mdima ndi kukufooketsa. Ngakhale zili choncho, ochuluka a m’nyumba yako, anthu adzawapha ndi lupanga.+ 1 Samueli 4:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ngakhalenso likasa la Mulungu linalandidwa,+ ndipo Hofeni ndi Pinihasi, ana awiri a Eli, anafa.+ 1 Samueli 22:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu.
33 Koma pali munthu wa m’nyumba yako amene sindidzamuchotsa paguwa langa lansembe kuti achititse maso ako mdima ndi kukufooketsa. Ngakhale zili choncho, ochuluka a m’nyumba yako, anthu adzawapha ndi lupanga.+
18 Pamapeto pake mfumu inauza Doegi+ kuti: “Iwe, tembenuka ukanthe ansembewa!” Nthawi yomweyo Doegi, Mwedomu,+ anatembenuka n’kukantha ndi kupha+ ansembewo tsiku limenelo, amuna 85 ovala efodi+ wa nsalu.