1 Samueli 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ndiyeno anthuwo atabwerera kumsasa, akulu a Isiraeli anayamba kunena kuti: “N’chifukwa chiyani lero Yehova watigonjetsa pamaso pa Afilisiti?+ Tiyeni tikatenge likasa la pangano la Yehova+ ku Silo, kuti likhale pakati pathu ndi kutipulumutsa m’manja mwa adani athu.” Salimo 78:61 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+ Maliro 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Yehova wachita zimene anali kuganiza.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wapasula zinthu ndipo sanamve chisoni.+Wachititsa adani ako kusangalala+ chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wakweza nyanga ya adani+ ako.
3 Ndiyeno anthuwo atabwerera kumsasa, akulu a Isiraeli anayamba kunena kuti: “N’chifukwa chiyani lero Yehova watigonjetsa pamaso pa Afilisiti?+ Tiyeni tikatenge likasa la pangano la Yehova+ ku Silo, kuti likhale pakati pathu ndi kutipulumutsa m’manja mwa adani athu.”
61 Analola kuti chizindikiro cha mphamvu zake chitengedwe ndi adani ake,+Iye analola kuti chizindikiro cha kukongola kwake chikhale m’manja mwa adani.+
17 Yehova wachita zimene anali kuganiza.+ Wakwaniritsa zimene ananena,+Zimene analamula kalekale.+ Wapasula zinthu ndipo sanamve chisoni.+Wachititsa adani ako kusangalala+ chifukwa cha zimene zakuchitikira. Wakweza nyanga ya adani+ ako.