Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ezekieli 5:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti, ‘Pali ine Mulungu wamoyo, chifukwa chakuti iwe unaipitsa malo anga opatulika ndi mafano ako onse onyansa+ ndi zinthu zako zonse zonyansa,+ ndithu ineyo ndidzakuchepetsa.+ Diso langa silidzakumvera chisoni+ ndipo sindidzakuchitira chifundo.+

  • Ezekieli 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Diso langa silidzakumverani chisoni+ ndipo sindidzakuchitirani chifundo.+ Ndidzakubwezerani mogwirizana ndi njira zanu, ndipo mudzaona zotsatirapo za zinthu zanu zonyansa zimene zili pakati panu.+ Ndiyeno anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova, amene ndikukuphani.+

  • Ezekieli 9:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Chotero inenso diso langa silimva chisoni+ ndipo sindichita chifundo.+ Ndiwabwezera mogwirizana ndi njira zawo.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena