Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 29:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Yehova sadzafuna kukhululukira+ munthu woteroyo, m’malomwake mkwiyo+ ndi ukali+ wa Yehova udzamuyakira,+ ndipo matemberero onse olembedwa m’buku+ ili adzakhala pa iye, motero Yehova adzafafanizadi dzina la munthuyo pansi pa thambo.

  • Ezekieli 7:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Diso langa silidzakumvera chisoni+ ndipo sindidzakuchitira chifundo. Ine ndidzakubwezera mogwirizana ndi njira zako, ndipo ukamadzalangidwa udzaona zotsatirapo za zinthu zako zonyansa zimene zili pakati pako.+ Chotero anthu inu mudzadziwa kuti ine ndine Yehova.’+

  • Ezekieli 8:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Choncho ineyo ndidzachitapo kanthu mwaukali.+ Diso langa silidzawamvera chisoni ndipo sindidzawachitira chifundo.+ Iwo adzandiitana mofuula, koma ine sindidzamva.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena