Deuteronomo 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako. Yeremiya 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Chotero ndisanawabwezeretse, ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse+ ndi machimo awo onse chifukwa choipitsa dziko langa.+ Anadzaza cholowa changa ndi mitembo ya zinthu zawo zochititsa mseru ndiponso zinthu zawo zonyansazo.’”+ Ezekieli 23:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Komanso anandichitira zinthu izi: Pa tsikulo anaipitsa+ malo anga opatulika+ ndiponso sabata langa.+
25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.
18 Chotero ndisanawabwezeretse, ndidzawabwezera zolakwa zawo zonse+ ndi machimo awo onse chifukwa choipitsa dziko langa.+ Anadzaza cholowa changa ndi mitembo ya zinthu zawo zochititsa mseru ndiponso zinthu zawo zonyansazo.’”+
38 Komanso anandichitira zinthu izi: Pa tsikulo anaipitsa+ malo anga opatulika+ ndiponso sabata langa.+