Numeri 35:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 “‘Musadetse dziko+ limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndiwo amadetsa dziko. Ndipo dziko lodetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe mwa njira ina, koma ndi magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+ Salimo 106:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+
33 “‘Musadetse dziko+ limene mukukhalamo, chifukwa magazi ndiwo amadetsa dziko. Ndipo dziko lodetsedwa ndi magazi silingayeretsedwe mwa njira ina, koma ndi magazi a munthu amene anakhetsa magaziyo.+
38 Choncho anali kukhetsa magazi a anthu osalakwa,+Magazi a ana awo aamuna ndi a ana awo aakazi,Amene anawapereka nsembe kwa mafano a ku Kanani.+Ndipo dzikolo linaipa ndi magazi amene iwo anakhetsa.+