Ekisodo 32:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Ndiyeno anatenga mwana wa ng’ombe amene iwo anapanga n’kumutentha ndi moto ndi kum’pera mpaka atakhala fumbi.+ Kenako anamwaza fumbilo pamadzi+ ndi kuwamwetsa Aisiraeli.+ Deuteronomo 12:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+ 1 Mbiri 14:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pa nthawiyi Afilisiti anasiya milungu yawo kumeneko.+ Ndiyeno Davide atalamula, milunguyo anaitentha pamoto.+
20 Ndiyeno anatenga mwana wa ng’ombe amene iwo anapanga n’kumutentha ndi moto ndi kum’pera mpaka atakhala fumbi.+ Kenako anamwaza fumbilo pamadzi+ ndi kuwamwetsa Aisiraeli.+
3 Mudzagwetse maguwa awo ansembe+ ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Mudzatenthe mizati yawo yopatulika+ ndi kudula zifaniziro zogoba+ za milungu yawo, ndipo mudzafafanize mayina awo pamalo amenewo.+
12 Pa nthawiyi Afilisiti anasiya milungu yawo kumeneko.+ Ndiyeno Davide atalamula, milunguyo anaitentha pamoto.+