Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 34:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Koma maguwa awo ansembe mukawagwetse, zipilala zawo zopatulika mukaziphwanye ndipo mizati yawo yopatulika mukaidule.+

  • 1 Mafumu 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Anachotsa ngakhalenso agogo ake aakazi a Maaka+ pa udindo wawo wokhala mayi wa mfumu,+ chifukwa anapanga fano lonyansa kwambiri+ lopembedzera mzati wopatulika. Pambuyo pake Asa anagwetsa fanolo n’kukalitentha+ m’chigwa* cha Kidironi.+

  • 2 Mafumu 23:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Inaphwanyaphwanya+ zipilala zopatulika ndipo inagwetsanso mizati yopatulika. Pamalo pamene panali zimenezi inadzazapo mafupa a anthu.

  • 2 Mbiri 14:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Choncho iye anachotsa maguwa ansembe achilendo,+ anagwetsa malo okwezeka,+ anaphwanya zipilala zopatulika+ ndi kudula mizati yopatulika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena