Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Oweruza 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Ndiyeno zinachitika kuti usiku womwewo, Yehova anauza Gidiyoni kuti: “Tenga ng’ombe yaing’ono yamphongo ya bambo ako, ng’ombe yachiwiri yazaka 7 ija. Kenako ugwetse guwa lansembe la Baala+ la bambo ako ndipo udule mzati wopatulika umene uli pafupi ndi guwalo.+

  • 2 Mafumu 18:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Hezekiya ndiye anachotsa malo okwezeka,+ kugwetsa zipilala zopatulika,+ ndi kudula mzati wopatulika.+ Iye anaphwanyaphwanya njoka yamkuwa+ imene Mose anapanga,+ chifukwa pofika masiku amenewo, ana a Isiraeli anakhala akufukiza nsembe+ yautsi kwa njoka yamkuwayo, ndipo inkatchedwa fano la njoka yamkuwa.+

  • 2 Mafumu 23:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Kuwonjezera apo, mfumuyo inatulutsa mzati wopatulika+ umene unali m’nyumba ya Yehova, ndipo inapita nawo kuchigwa* cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu n’kukautentha+ kuchigwacho. Itatero, inauperapera n’kuwaza fumbi lake pamanda+ a ana a anthu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena