Numeri 21:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Upange chifanizo cha njoka yapoizoni* ndipo uchiike pamtengo wachizindikiro. Munthu aliyense amene walumidwa, akayang’ana njokayo akhalebe ndi moyo.”+
8 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Upange chifanizo cha njoka yapoizoni* ndipo uchiike pamtengo wachizindikiro. Munthu aliyense amene walumidwa, akayang’ana njokayo akhalebe ndi moyo.”+