Miyambo 15:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Nsembe ya anthu oipa imam’nyansa Yehova,+ koma pemphero la anthu owongoka mtima limam’sangalatsa.+