Deuteronomo 7:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako. Deuteronomo 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Ndipo mwana wa ng’ombeyo,+ amene munachimwa pomupanga, ndinamutenga n’kumutentha ndi moto ndi kumuphwanya, n’kumupera mpaka atakhala wosalala ngati fumbi. Kenako ndinamwaza fumbilo mumtsinje wotuluka m’phirimo.+
25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.
21 Ndipo mwana wa ng’ombeyo,+ amene munachimwa pomupanga, ndinamutenga n’kumutentha ndi moto ndi kumuphwanya, n’kumupera mpaka atakhala wosalala ngati fumbi. Kenako ndinamwaza fumbilo mumtsinje wotuluka m’phirimo.+