Ekisodo 23:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+ Numeri 33:52 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+ 2 Mafumu 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Inaphwanyaphwanya+ zipilala zopatulika ndipo inagwetsanso mizati yopatulika. Pamalo pamene panali zimenezi inadzazapo mafupa a anthu.
24 Usaweramire milungu yawo kapena kuitumikira, ndipo usapange chilichonse chofanana ndi zifaniziro zawo,+ koma uzigwetse ndithu ndi kuphwanya zipilala zawo zopatulika.+
52 Mukapitikitse anthu onse a m’dzikolo, ndipo mukawononge zifaniziro zawo zonse zamiyala,+ ndi mafano awo onse achitsulo.+ Mukawonongenso malo awo onse opatulika olambirira.+
14 Inaphwanyaphwanya+ zipilala zopatulika ndipo inagwetsanso mizati yopatulika. Pamalo pamene panali zimenezi inadzazapo mafupa a anthu.