6 Kuwonjezera apo, mfumuyo inatulutsa mzati wopatulika+ umene unali m’nyumba ya Yehova, ndipo inapita nawo kuchigwa cha Kidironi kunja kwa mzinda wa Yerusalemu n’kukautentha+ kuchigwacho. Itatero, inauperapera n’kuwaza fumbi lake pamanda+ a ana a anthu.