Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndiyeno anatenga mwana wa ng’ombe amene iwo anapanga n’kumutentha ndi moto ndi kum’pera mpaka atakhala fumbi.+ Kenako anamwaza fumbilo pamadzi+ ndi kuwamwetsa Aisiraeli.+

  • Deuteronomo 7:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Mudzatenthe zifaniziro zogoba za milungu yawo.+ Usadzalakelake siliva ndi golide wawo+ kapena kudzitengera zinthu zimenezi,+ kuopera kuti zingakutchere msampha,+ chifukwa zimenezi ndi zonyansa+ kwa Yehova Mulungu wako.

  • 2 Mafumu 19:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Atentha milungu yawo pamoto, chifukwa sinali milungu,+ koma ntchito ya manja a anthu,+ mitengo ndi miyala, n’chifukwa chake anaiwononga.

  • 1 Akorinto 10:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ndiye chifukwa chake, okondedwa anga, thawani+ kupembedza mafano.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena