Yeremiya 15:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndani adzakusonyeza chifundo, iwe Yerusalemu? Ndani adzakumvera chisoni+ ndipo ndani adzapatuka ndi kufunsa za moyo wako?’
5 Ndani adzakusonyeza chifundo, iwe Yerusalemu? Ndani adzakumvera chisoni+ ndipo ndani adzapatuka ndi kufunsa za moyo wako?’