Salimo 69:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha chitonzo, ndipo chilonda chake ndi chosachiritsika.+Ndinali kuyembekezera kuti wina andimvere chifundo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndinali kuyembekezera onditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+ Yesaya 51:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Zinthu ziwiri zidzakugwera.+ Kodi adzakumvera chisoni ndani?+ Udzalandidwa katundu ndi kuphwanyidwa, ndiponso udzakumana ndi njala ndi lupanga.+ Kodi adzakutonthoza ndani?+ Maliro 1:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Inu nonse amene mukudutsa m’njira, kodi mukuona ngati imeneyi ndi nkhani yaing’ono? Ndiyang’aneni kuti muone.+Kodi palinso ululu wina woposa ululu umene ineyo ndalangidwa nawo,+Ululu umene Yehova wandibweretsera nawo chisoni m’tsiku la mkwiyo+ wake woyaka moto?
20 Mtima wanga wasweka chifukwa cha chitonzo, ndipo chilonda chake ndi chosachiritsika.+Ndinali kuyembekezera kuti wina andimvere chifundo, koma panalibe ndi mmodzi yemwe,+Ndinali kuyembekezera onditonthoza, koma sanapezeke ngakhale mmodzi.+
19 Zinthu ziwiri zidzakugwera.+ Kodi adzakumvera chisoni ndani?+ Udzalandidwa katundu ndi kuphwanyidwa, ndiponso udzakumana ndi njala ndi lupanga.+ Kodi adzakutonthoza ndani?+
12 Inu nonse amene mukudutsa m’njira, kodi mukuona ngati imeneyi ndi nkhani yaing’ono? Ndiyang’aneni kuti muone.+Kodi palinso ululu wina woposa ululu umene ineyo ndalangidwa nawo,+Ululu umene Yehova wandibweretsera nawo chisoni m’tsiku la mkwiyo+ wake woyaka moto?