Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 32:41
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 41 Ndikanoladi lupanga langa lonyezimira,+

      Dzanja langa likagwira chiweruzo,+

      Ndidzalipsira adani anga,+

      Ndipo ndidzabwezera chilango kwa odana nane kwambiri.+

  • 2 Mbiri 6:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 inu mumve muli kumwamba+ ndipo muchitepo kanthu+ mwa kusonyeza amene ali wolakwa pom’bwezera temberero lake,+ ndi kusonyeza amene ali wolungama+ pom’patsa mphoto malinga ndi chilungamo chake.+

  • Ezekieli 11:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 “‘“Koma amene akuumirira mafano awo onyansa ndi zinthu zawo zonyansa,+ ndidzawabwezera monga mwa njira zawo,” watero Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa.’”+

  • Aheberi 10:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Pakuti timamudziwa amene anati: “Kubwezera ndi kwanga, ndidzabwezera ndine.”+ Ndiponso: “Yehova adzaweruza anthu ake.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena