Maliro 2:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Anyamata ndi amuna okalamba+ agona pansi m’misewu.+Anamwali anga ndi anyamata anga aphedwa ndi lupanga.+Mwapha anthu pa tsiku la mkwiyo+ wanu. Onsewo mwawaphadi+ mopanda chisoni.+ Zekariya 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “‘Sindidzachitiranso chifundo anthu okhala m’dzikoli,’+ watero Yehova. ‘Choncho ine ndichititsa aliyense kuti aponderezedwe ndi mnzake+ ndiponso mfumu yake.+ Iwo adzawononga dzikoli, ndipo ine sindidzapulumutsa aliyense m’manja mwawo.’”+
21 Anyamata ndi amuna okalamba+ agona pansi m’misewu.+Anamwali anga ndi anyamata anga aphedwa ndi lupanga.+Mwapha anthu pa tsiku la mkwiyo+ wanu. Onsewo mwawaphadi+ mopanda chisoni.+
6 “‘Sindidzachitiranso chifundo anthu okhala m’dzikoli,’+ watero Yehova. ‘Choncho ine ndichititsa aliyense kuti aponderezedwe ndi mnzake+ ndiponso mfumu yake.+ Iwo adzawononga dzikoli, ndipo ine sindidzapulumutsa aliyense m’manja mwawo.’”+