Yeremiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+ Yeremiya 18:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Chotero ana awo muwakhaulitse ndi njala yaikulu,+ ndipo aphedwe ndi lupanga.+ Akazi awo akhale amasiye ndipo ana a akaziwo afe.+ Amuna awo afe ndi mliri woopsa ndipo anyamata awo aphedwe ndi lupanga pa nkhondo.+ Maliro 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+
21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+
21 Chotero ana awo muwakhaulitse ndi njala yaikulu,+ ndipo aphedwe ndi lupanga.+ Akazi awo akhale amasiye ndipo ana a akaziwo afe.+ Amuna awo afe ndi mliri woopsa ndipo anyamata awo aphedwe ndi lupanga pa nkhondo.+
15 Yehova wandichotsera anthu anga onse amphamvu+ ndi kuwakankhira pambali.Wandiitanitsira msonkhano kuti athyolethyole anyamata anga.+Yehova wapondaponda moponderamo mphesa+ mwa namwali, mwana wamkazi wa Yuda.+