2 Mbiri 36:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake. Yeremiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+
17 Choncho anawabweretsera mfumu ya Akasidi+ yomwe inapha anyamata awo ndi lupanga+ m’nyumba yopatulika.+ Sinachitire chisoni mnyamata kapena namwali, wachikulire kapena nkhalamba yotheratu.+ Mulungu anapereka zonse m’manja mwake.
21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+