Deuteronomo 32:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+ Maliro 5:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ife takhala anthu amasiye opanda bambo.+ Amayi athu akhala ngati akazi amasiye.+
25 Kunja lupanga lidzawasandutsa anamfedwa,+Ndipo mkati mwa nyumba, mantha adzawasandutsa anamfedwa.+Zimenezi zidzawaphera anyamata ndi anamwali,+Mwana woyamwa pamodzi ndi munthu wa imvi.+