Yeremiya 9:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+ Maliro 1:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Taonani, inu Yehova. Inetu zandivuta. M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Mtima wanga wasweka,+ pakuti ndapanduka kwambiri.+Panja, lupanga lapha+ ana. M’nyumba, anthu akufanso.+
16 Ndidzawamwaza pakati pa mitundu ya anthu imene iwo kapena makolo awo sanaidziwe.+ Ndidzawakantha ndi lupanga kufikira nditawafafaniza.’+
20 Taonani, inu Yehova. Inetu zandivuta. M’mimba mwanga mukubwadamuka.+Mtima wanga wasweka,+ pakuti ndapanduka kwambiri.+Panja, lupanga lapha+ ana. M’nyumba, anthu akufanso.+