-
Ezekieli 5:2Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
2 Gawo limodzi la magawo atatu a tsitsilo ulitenthe pamoto pakati pa mzindawo masiku ozungulira mzindawo akatha.+ Kenako utenge gawo lina la magawo atatuwo. Gawo limeneli uzilimenya ndi lupanga ukuzungulira mzinda wonsewo.+ Gawo lomaliza la magawo atatuwo uliuluze ndi mphepo ndipo ine ndidzalitsatira nditasolola lupanga.+
-