Yeremiya 9:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+ Ezekieli 4:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ine ndidzakumanga ndi zingwe+ kuti usatembenukire kumbali ina, mpaka utamaliza masiku ako ozungulira mzindawo.
21 Pakuti imfa yatilowera m’nyumba kudzera m’mawindo. Yalowa munsanja zathu zokhalamo kuti mumsewu musapezeke mwana aliyense ndiponso kuti anyamata asapezeke m’mabwalo a mzinda.’+
8 “Ine ndidzakumanga ndi zingwe+ kuti usatembenukire kumbali ina, mpaka utamaliza masiku ako ozungulira mzindawo.