-
Deuteronomo 28:61Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
61 Kuwonjezera pamenepo, Yehova adzakubweretsera nthenda iliyonse ndi mliri uliwonse umene sunalembedwe m’buku la chilamulo ili, kufikira utafafanizika.
-
-
Yeremiya 34:17Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
17 “Choncho Yehova wanena kuti, ‘Inu simunamvere mawu anga moti simunapitirize kulengeza ufulu,+ aliyense kwa m’bale wake ndi kwa mnzake. Tsopano ine ndikulengeza ufulu kwa inu,’+ watero Yehova. ‘Inu mudzafa ndi lupanga,+ mliri+ ndi njala yaikulu.+ Ndidzakusandutsani chinthu chimene maufumu onse a padziko lapansi adzanthunthumira nacho.+
-